Oyimba wa Ku Malawi Mr Thompo walimbikitsa oyimba a mdziko la South Africa
Oyimba wa Ku Malawi Mr Thompo walimbikitsa oyimba a mdziko la South Africa amene anachoka ku mudzi ku Malawi ndipo tsopano akuyimba mdzikoli pamene walankhula ndi Stella Longwe pa pologalamu ya Malonje.
Oyimba wa ku Malawi Master Manda waonetsa kuti khama limapindula
Oyimba wa ku Malawi amene akukhala mdziko la South Africa,Master Manda, waonetsa kuti khama limapindula pamene anayamba kuyimba ndi zida za lokolo zopanda magetsi ndipo pano amayimba ndi zida za magetsi. Iye akuyembekezeka kutulutsa chimbale masiku akubwelawa.
Malonje
Mupologalamuyi muli nyimbo zosiyana siyanan za mu Africa komanso tacheza ndi oyimba wa mdziko la Malawi amene ali mdziko la South Africa, Andrew Mbalasa .
Malonje
Mu pologalamuyi muli nyimbo zosiyana siyana za mu Africa komanso omvela apeleka malonje kwa okondedwa awo.
Malonje 09 March 2024
Malonje
Nyimbo zosiyana siyana za mu Africa zaseweledwa mu pulogalamuyi, komanso omvela apeleka moni kwa abale ndi okondedwa awo.
Malonje
Pologalamu imeneyi ili ndi nyimbo zosiyana siyana za mu Africa komanso Muwulutsi wa Polagalamuyi Stella Longwe wacheza ndi katswili oyimba wa mdziko la Mozambique Buscade Kawaza.
Malonje
Pologalamu ya Malonje imakhala ndi nyimbo zosiyana siyana za mu Africa komanso omvela amapeleka moni kwa okondwedwa awo.
Malo
Program ya malonje imene imabwela loweluka ndipo omvela amapeleka moni kwa okondwedwa awo komanso mu programuyi mumakhala nyimbo za mayiko osiyana siyana a mu Africa.
Malonje
Program ya malonje imene imabwela loweluka ndipo omvela amapeleka moni kwa okondwedwa awo komanso mu programuyi mumakhala nyimbo za mayiko osiyana siyana a mu Africa.