Pali kugawikana maganizo pakati pa boma la zambia ndi mgwilizano wa zipani zosutsa boma wa Tonse Alliance za ku malo oli-li-ra maliro a prezidenti wakale wa Zambia Edgar Chagwa Lungu pamene boma la dzikolo layimitsa kuti thupi la malemu Lungu linyamuke kuchoka mdziko la South Africa kupita ku Zambia lero. Ziyenela Zimba wabwela ndi tsatane tsatane wa nkhaniyi.

Oyimba wa mdziko la Mozambique BS Music wati oyimba asamayike maso pa ndalama
13:35

Mada Phiri kucheza ndikatswili oyimba wa mdziko la DRC Feed Paul RP amene amadziwika
13:05

Oyimba wa manganje wa ku Mozambique Ricabana wati amanyadila kuyimba za chimidzi
10:48