Oyimba wa manganje wa ku Mozambique Ricabana, wati amanyadila kuyimba za chimidzi ndipo apitilira kuyimba nyimbo za chikhalidwe ngakhale akukumana ndi mavuto osiysa siyana. Stella Longwe walankhula ndi oyimbayu pa programu ya Malonje

Mada Phiri kucheza ndikatswili oyimba wa mdziko la DRC Feed Paul RP amene amadziwika
13:05

Gulu la akatswili opanga ndikusoka zovala zosiyana siyana la PSV Luxury, ladziko la Malawi koma amakhala mdziko la South Africa, kucheza ndi Mada Phiri ndikutiuza mmene anayambila ntchito yawo
23:48

MONEY MIKE INTERVIEW
16:25