Oyimba wa Ku Malawi amene amakhala mdziko la South Africa L Nowa, wati oyimba asamamvele zokamba kamba koma azipita chitsogolo kuti azipitilira ndi luso lawo loyimba. Stella Longwe anacheza ndi oyimbayu pa program ya Malonje

Oyimba wa mdziko la Mozambique BS Music wati oyimba asamayike maso pa ndalama
13:35

Mada Phiri kucheza ndikatswili oyimba wa mdziko la DRC Feed Paul RP amene amadziwika
13:05

Oyimba wa manganje wa ku Mozambique Ricabana wati amanyadila kuyimba za chimidzi
10:48