Kucheza ndi katswili wazoimba imba wadziko la South Africa Money Mike, pamene watiuza kuti wapanga ngwilizano ndi nyumba yaikulu yojambula nyimbo yaku America ya Sonny komaso ya Rico Nation, ndi kutulutsa nyimbo yake yotchedwa Alhamdulila.

Oyimba wa mdziko la Mozambique BS Music wati oyimba asamayike maso pa ndalama
13:35

Mada Phiri kucheza ndikatswili oyimba wa mdziko la DRC Feed Paul RP amene amadziwika
13:05

Oyimba wa manganje wa ku Mozambique Ricabana wati amanyadila kuyimba za chimidzi
10:48