Malonje (Chinyanja)Malonje (Chinyanja)

Kucheza ndi Starval oyimba wa ku Malawi

View descriptionShare

Katswili oyimba wa ku Malawi amene akuyimba mdziko la South Africa Starval Stevens, wati chidwi choyimba ndi chomwe chimapangitsa oyimba kuti apitilire kuyimba ngakhale akukumana ndi zovuta zambiri. Stella Longwe wacheza ndi katswiliyu.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back 
Recent clips
Browse 44 clip(s)