Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Wachiwiri kwa President wa Kenya Rigathi Gachagua wachotsedwa udindo

View descriptionShare

Wachiwiri kwa  a pulezident wa dziko la Kenya a Rigathi Gachagua amuchotsa pa udindo. Izi zikutsatira pomwe aphungu anavoterabe kuti a Gachagua atule pansi udindo wawo kamba ka milandu khumi ndi umodzi, 11 yomwe amawazenga. Mtolankhani nzathu kum’mawa kwa Africa, Alfred Dzaoneni ali ndi zambiri.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    532 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 670 clip(s)