Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Kwatsala masiku awiri kuti anthu mdziko la Mozambique aponye voti

View descriptionShare

Katswili owona zochitika mu Africa, Dr Griffin Maruwasa  wati masankho amene anthu a mdziko la Mozambique adzachite lachitatu pa 9 October chaka chino akuwonetsa kuti demokalase ikuyenda bwino mdzikolo. Stella Longwe walankhula ndi Katswiliyu.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    532 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 670 clip(s)