Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Dziko la Zambia lakweza nambala ya anthu olandila ndalama kuchokela ku boma

View descriptionShare

Boma la Zambia lakweza   chiwelengelo cha anthu olandila ndalama pansi pa ndondomeko ya Social Cash Transfer kufika pa anthu 1.3 million kuchoka pa anthu oposela pang’ono 600,000 ndipo  ndalamazi zimapelekedwa kwa anthu okalamba, ana amasiye  olelana okha okha,  anthu a ulumali, amayi omwe ndi osakwatiwa koma ali ndi ana atatu kupita mtsogolo ndi anthu omwe akudwala kwambiri, ziyenela zimba wadza ndi nkhani yonse

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    532 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 670 clip(s)