Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

President wa Malawi Lazarus Chakwera wati dzikolo walimbikitsa ntchito za migodi

View descriptionShare

President wa dziko la Malawi Lazarus Chakwera wati dzikolo lili ndi miyala yamtengo wapatali yambiri yomwe ingathandizire kukweza chuma  cha dzikolo, ngati maiko ena angagule miyalayo.

Izitu zadziwika lero pamwamba  pa msonkhano wa mining investment forum omwe ukuchitikira munzinda wa Lilongwe mdzikolo.

Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    532 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 670 clip(s)