Mtsogoleri wachipani chotsutsa boma cha National Unity Platform NUP ku Uganda a Robert Chagulanyi Sentamu omwe amadziwikanso kuti Bobi Wine atuluka m'dziko la Uganda. Zifukwa zeni zeni zomwe iwo atulukira mdzikolo sizikudziwika koma a Bobi Wine akhala akunena kuti moyo wawo unali pa chiopsyezo ndi asilikali ankhondo adzikoli chimalizireni chisankho m'mwezi wa January chaka chino. Alfred Dzaoneni yemwe ndi Mtolankhani mzathu kum'mawa kwa Africa akufotokoza zambiri.

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11

Mchitidwe wa uchifwamba ukuchulukila ku Malawi
06:53