Pambuyo pakubedwa kwa mwini wa crossroads hotel ku Lilongwe mdziko la Malawi, tsopano anthu ayamba kumasowa, ena kubedwa kumene, pomwenso ena akumapezeka ataphedwa patapita masiku. Ena akumawaba nkukawagwi-li-li-ra atawamwetsa mankhwala ogonetsa. Jayne Chilimampunga wabwela ndi nkhani yonse.

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11

Mtsogoleri wa Zambia Hakainde Hichilema wati amayi ndi ofunikila kwambiri
09:57

Mpungwe pungwe wabuka mchipani chotsutsa boma ku Malawi cha MCP
06:45