Mpungwepungwe wabuka mchipani chotsutsa boma cha Malawi Congress Party--MCP mdziko la Malawi pomwe kagulu kena kakufuna mtsogoleri wa Chipanichi Dr Lazarus Chakwera kuti atule pansi udindo wawo pomwe ena akuti kaguluko kangotumidwa chabe. Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11

Mchitidwe wa uchifwamba ukuchulukila ku Malawi
06:53

Mtsogoleri wa Zambia Hakainde Hichilema wati amayi ndi ofunikila kwambiri
09:57