Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mtsogoleri wa Zambia Hakainde Hichilema wati amayi ndi ofunikila kwambiri

View descriptionShare

Mtsogoleri wa dziko la Zambia Hakainde Hichilema, wafotokoza kuti azimai ndi nsanamira zofunikira kwambiri pa zitukuko za dziko.  A Hichilema analankhula mauwa dzulo pa mwambo wokumbukira tsiku la amai pa dziko lonse lapansi limene cha pamutu chake chinali motere: Danga, Chilungamo, Kuchitapo Kanthu, Kwa Amai ndi Atsikana Onse . Daniel Elisha Banda ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 955 clip(s)