President wa dziko la Zambia Hakainde Hichilema wachotsa ntchito nduna ya za umoyo, a Elijah Muchima ndi nduna ya ntchito za malonda zing'ono-zing'ono, a Elias Mubanga ndipo mkulu yemwe amafalitsa nkhani zaku nyumba ya boma ya President, Clayson Hamasaka, ndi amene walengeza nkhaniyi mu chikalata chake. Daniel Elisha Banda akulongosola zambiri.

Mary Chilima wayamikila Mutharika mtsogoleri wa Malawi pofufuza imfa ya Chilima
08:31

Kachilombo ka Polio 2 kapezeka mu mzinda wa Lusaka ku Zambia
05:48

Zipani zina zotsutsa boma ku Zambia sizikufuna kuwonjezela aphungu 70
08:17