Kachilombo ka matenda a Polio type 2 kapezeka mu mzinda wa Lusaka mdziko la Zambia ndipo kachilomboka kakufanana ndi kachilombo kamene kanapezeka m’mayiko a Namibia ndi Angola. Ziyenela Zimba wabwela ndi nkhani yonse

Mary Chilima wayamikila Mutharika mtsogoleri wa Malawi pofufuza imfa ya Chilima
08:31

Mtsogoleri wa Zambia Hakainde Hichilema wachotsa nduna ziwiri
08:43

Zipani zina zotsutsa boma ku Zambia sizikufuna kuwonjezela aphungu 70
08:17