Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mary Chilima wayamikila Mutharika mtsogoleri wa Malawi pofufuza imfa ya Chilima

View descriptionShare

Mayi Mary Chilima mkazi wa yemwe anali wachiwiri kwa President wa dzikolo Dr Saulos Klaus Chilima wayamikila ganizo la mtsogoleri wa dzikolo Professor Arthur Peter Mutharika lokuti pakhalenso kafufuku wina wa ngozi ya ndege yomwe inapha a Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu (8) m' mwezi wa June mchaka cha 2024. George wabwera ndi tsatane tsatane wa nkhaniyi
 

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 946 clip(s)