Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mayiko a Zimbabwe, Zambia ,Malawi agwilizana zochotsa msonkho wa lamya

View descriptionShare

Mayiko  a Zimbabwe, Zambia Malawi ndi Botswana agwilizana zochotsa ndalama ya msonkho imene anthu amalipila akamagwilitsa ntchito ma telephoni a mmanja  akakhala ku mayiko a chilendo.

John Kassim akusimba....

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 960 clip(s)