Raphael Tuju, yemwe ndi Nduna yakale yoona za ubale pakati pa dziko la Kenya ndi mayiko ena , amupeza ndipo amumanga kamba konamilizira kuti wasowa komanso kuti anabedwa.Mkulu wotsogolera kafukufuku ku polisi ya Nairobi a Mohamed Amin, anena pa msonkhano wa atolankhani kuti a Tuju anali mkati mwa nyumba yake nthawi yonseyi, ndipo anafotokoza kuti kusowa kwa Tuju kunali kokonzedwa mwadala osati kubedwa ndi anthu achipongwe. Mtolankhani mzathu ku m'mawa kwa Africa Alfred Dzaoneni ali ndi zambiri.

Mafuta agalimoto akwera ku Malawi ndi 35%
06:44

Anthu 300 amangidwa ku Zambia Kamba kopha mayi wina pomuganizila kuti ndi mfiti
08:47

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07