Mafuta a galimoto ndi ndege akwera kwambiri mdziko la Malawi zomwe zikupereka chiopsezo kuti mwina zinthu zofunikila pamoyo wa anthu zikwera mtengo. Mafuta a petrol akwera ndi 34 % kufika pa K6,672 kuchoka pa K4,935 ndipo Dizilo wakwela ndi 35% kufika pa mtengo wa K6,687 kuchoka pa K4,945 . Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse

Anthu 300 amangidwa ku Zambia Kamba kopha mayi wina pomuganizila kuti ndi mfiti
08:47

Apolisi ku Kenya amanga nduna yakale chifukwa chonamizila kubedwa
06:05

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07