Ntchito yomanga fakitole yopanga fetereza ikupita kumapeto tsopano mdziko la Malawi. Fakitoleyi ikumangidwa ndi katswiri ochita za malonda Dr Nepoleon Dzombe. Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

Anthu ena ozapisikana pa masankho ku Zambia ali ndi masatifiketi abodza
09:02

Atsikana achichepele ambiri akumazipeleka kwa azibambo ku Malawi
06:52

Bungwe la IBA ku Zambia latulutsa malamulo a kufalitsa nkhani za masankho
08:29