Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Bungwe la IBA ku Zambia latulutsa malamulo a kufalitsa nkhani za masankho

View descriptionShare
 

Bungwe la Independent Broadcasting Authority la dziko la Zambia la  IBA, latulutsa malamulo atsopano okhudza momwe mawayilesi ndi ma TV ayenera kufalitsira nkhani za chisankho cha dzikolo cha mchaka cha 2026. Mkulu wa  bungweli, Webster Malido, wafotokoza kuti malamulowa akhazikitsidwa pofuna kulimbikitsa chilungamo, kusakondera komanso kuteteza mtendere pa nthawi ya kampeni ndi chisankho . Tili ndi zambiri mu lipoti la Daniel Elisha Banda.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 986 clip(s)