Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Anthu ena ozapisikana pa masankho ku Zambia ali ndi masatifiketi abodza

View descriptionShare
 

Bungwe la Examinations Council of Zambia, ECZ, lati lapeza ma certificate 10 abodza a Grade 12 kuchokera kwa anthu ena amene akufuna kudzapikisana pa zisankho za pa 13 August 2026. Nkhaniyi yabweretsa nkhawa pakati pa nzika pamene malamulo a dziko la Zambia amafuna kuti munthu aliyense amene akufuna kutenga nawo mbali pa zisankho akhale ndi satifiketi ya Grade 12 ngati chimodzi mwa ziyenerezo zofunikira. Daniel Elisha Banda akutambasula nkhaniyi.
 

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 986 clip(s)