Asungwana ambiri achichepele mdziko la Malawi, akumazipeleka kwa azibambo kuti aziwazembetsa kuti azigulitsa matupi awo chifukwa cha umphawi ndi kusazindikila. Jayne Chilimampunga akutambasula nkhaniyi.

Anthu ena ozapisikana pa masankho ku Zambia ali ndi masatifiketi abodza
09:02

Fakitole yopanga feteleza ku Malawi ya a Dzombe ikupita kumapeto
07:38

Bungwe la IBA ku Zambia latulutsa malamulo a kufalitsa nkhani za masankho
08:29