Boma la dziko la Malawi lakana kubweleka ndalama zochuluka kwa ochita malonda ndi makampani a mdzikolo chifukwa likufuna kubweza ngongole zomwe lili nazo kale . George Mhango akusimba

Mafuta agalimoto akwera ku Malawi ndi 35%
06:44

Anthu 300 amangidwa ku Zambia Kamba kopha mayi wina pomuganizila kuti ndi mfiti
08:47

Apolisi ku Kenya amanga nduna yakale chifukwa chonamizila kubedwa
06:05