Anthu ambiri akufuna kuti boma likhazikitse lamulo loti opha nzake naye aziphedwa, ndikuti president azisainira.Izi zadza pamene mchitidwe ophana chisawawa ukunka nuchulukira ku Malawi. Sabata yatha ku Mwanza anthu anapeza mafupa a ana aakazi awiri wina zaka 10 wina 12 mminda yosiyana, atasowa kwa masiku ambiri. Jayne Chilimampunga wadza ndi nkhaniyi

Mafuta agalimoto akwera ku Malawi ndi 35%
06:44

Anthu 300 amangidwa ku Zambia Kamba kopha mayi wina pomuganizila kuti ndi mfiti
08:47

Apolisi ku Kenya amanga nduna yakale chifukwa chonamizila kubedwa
06:05