Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi

View descriptionShare

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
783 clip(s)
Loading playlist

Mchitidwe ochitila nkhanza anthu a chi Alubino wayambilanso m’madela ena a mdziko la Malawi ndipo mtsogoleri wa bungwe la APAM la anthu a chi alubino Young  Muhamba, wati akufuna kuti akadandaule za mchitidwewu kwa mtsogoleri wa dzikolo Professor Arthur Peter Mutharika. Jayne Chilimampunga akutambasula bwino nkhaniyi.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 926 clip(s)