Akatswili osiyana siyana a mdziko la Malawi, alankhulapo pa za mtsogoleri wa dzikolo professor Arthur Peter Mutharika, kukwanitsa masiku 100 chiyambileni kulamula pambuyo popambana masankho chaka chatha. George Mhango akusimba.

Tonse Alliance ku Zambia yawina masankho a dela Chawama
07:32

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi
07:17

Alimi ena ku Zambia akudikilabe boma liwapatse malipiro atagulitsa mbewu ku FRA
07:55