Alimi ambiri mdziko la Zambia, akudandaula kuti boma likuchedwa kuwapatsa ndalama zawo pa zokolola zawo zomwe anagulitsa ku bungwe la boma lowona za chakudya la Food Reserve agency chaka chatha pamene boma linalonjeza kuti liwalipira alimi onse a mdzikolo pofika pa 10 January chaka chino. Ziyenela Zimba wabwela ndi nkhani yons

Tonse Alliance ku Zambia yawina masankho a dela Chawama
07:32

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi
07:17

Akatswili a ndale ati A Mutharika akutsogolera bwino Malawi
06:24