Yemwe kale anali Nduna ya za chuma mdziko la Mozambique Manuel Chang, wapita ku bwalo la Federal mdziko la USA pa kufuna kuti limve pempho lake lofuna kuti atulutsidwe mndende. Bright Sonjera akufotokoza

Tonse Alliance ku Zambia yawina masankho a dela Chawama
07:32

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi
07:17

Alimi ena ku Zambia akudikilabe boma liwapatse malipiro atagulitsa mbewu ku FRA
07:55