Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Anthu 7  aphedwa ku Malawi pogawaganizila kuti akusowetsa maliseche

View descriptionShare
 

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
832 clip(s)
Loading playlist

Anthu asanu ndi awiri (7)aphedwa  masiku apitawa m’maboma a Chikwawa ndi Nsanje mdziko la Malawi powaganizila kuti anasowetsa maliseche a anthu ena. Jayne Chilimampunga ali ndi nkhaniyi 

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 975 clip(s)