Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Venancio Mondlane wati anthu alile maliro a Anselmo Vicente ku Mozambique

View descriptionShare
 

Mtsogoleri wa chipani chosutsa boma mdziko la Mozambique cha Anamola Venancio Mondlane, wapempha kuti pakhale masiku atatu olira maliro a m’modzi mwa akulu akulu a chipanichi Anselmo Vicente  amene anaphedwa loweluka lapitali  mtawuni ya Chimoio mchigawo cha Manica. Bright Sonjela akufotokoza tsatane tsatane wa nkhaniyi.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 975 clip(s)