Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Bungwe la CHREA ku Malawi likufuna kuti akaidi azichita za dama ndi akazi awo

View descriptionShare
 

Pali maganizo osiyana  mdziko la Malawi pa za ufulu wa akaidi oti azipatsidwa mpata okhala malo amodzi ndi okondedwa awo pa nthawi yomwe akuphika ndende mdziko la Malawi. Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 975 clip(s)