Anthu a ku m’mwela kwa dziko la Mozambique maka maka mchigawo cha Inhambane, akhuzidwa kwambili ndi namondwe wa Gezani pamene anthu oposela 17,000 alibe magetsi komanso mabanja 880 akusowelatu pokhala. Bright Sonjela akufotokoza Zambiri

Mafuta agalimoto akwera ku Malawi ndi 35%
06:44

Anthu 300 amangidwa ku Zambia Kamba kopha mayi wina pomuganizila kuti ndi mfiti
08:47

Apolisi ku Kenya amanga nduna yakale chifukwa chonamizila kubedwa
06:05