Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Zipolowe zikuchitika ku misonkhano ina ya ndale yokopa anthu ku Malawi

View descriptionShare
 

Ku misonkhano ina ya ndale yokopa anthu mdziko la Malawi  kukuchitika  zipolowe pamene zipani zayamba kuchita kampeni pokonzekela masankho omwe adzachitike chaka cha mmawa mdzikolo. Jane Chilimampunga ali ndi nkhani yonse

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 975 clip(s)