Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko la Malawi Dr Micheal Usi, ati boma lalanda galimoto imodzi yomwe amayendera ngati wachiwiri wa dzikolo komanso iwo ati ena awachenjeza kuti akufuna kupangidwa chiwembu akapita ku Lilongwe. Kondwani Nyamasauka akufotokoza tsatane-tsatane wa nkhani yonse.

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11

Mchitidwe wa uchifwamba ukuchulukila ku Malawi
06:53