Mtsogoleri wa chipani chosutsa boma mdziko la Mozambique cha Anamola Venancio Mondlane, wapempha kuti pakhale masiku atatu olira maliro a m’modzi mwa akulu akulu a chipanichi Anselmo Vicente amene anaphedwa loweluka lapitali mtawuni ya Chimoio mchigawo cha Manica. Bright Sonjela akufotokoza tsatane tsatane wa nkhaniyi.

AIPAC ku Zambia yatsuta kuwunika ma bilu pomwe paliyamenti itseke pa 15 May 2026
10:17

Anthu 7 aphedwa ku Malawi pogawaganizila kuti akusowetsa maliseche
05:25

Bungwe la CHREA ku Malawi likufuna kuti akaidi azichita za dama ndi akazi awo
07:53