Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Unduna owona za ntchito ku Malawi ukulimbikitsa ma ufulu a anthu ogwila ntchito

View descriptionShare

 Nduna yowona za ntchito mdziko la Malawi olemekezeka a  Peter Dimba, ati unduna wawo upitilira kuyendela ma makampani osiyana siyana mdzikolo pofuna kuwonesetsa kuti ma ufulu a ogwila ntchito azilemekezedwa ndi kutetezedwa pamene mayiko pa dziko lonse la pansi akukumbukila anthu ogwila ntchito. Thamo Kapisa wabwela ndi nkhaniyi.

 

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 957 clip(s)