Boma la Zambia lagwilizana ndi banja la malemu Edgar Lungu yemwe anali president wakale wa dziko la Zambia zokuti boma lidzachita mwambo wa maliro a Lungu pambuyo pa kusamvana pakati pa mbali ziwirizi ndipo thupi la a Lungu lizanyamuka mdziko la South Africa kupita ku Zambia lachitatu sabata ino pa 18 June. Ziyenela Zimba wabwela ndi tsatane tsatane wa nkhaniy

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11