Presidenti wa dziko la Malawi, Professor Arthur Peter Mutharika, wasintha nduna zake za boma patangodutsa miyezi itatu iye kukhala mtsogoleri wa dzikolo. Mtolankhani wa Channel Africa George Mhango wafotokoza zambiri.

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi
07:17

Alimi ena ku Zambia akudikilabe boma liwapatse malipiro atagulitsa mbewu ku FRA
07:55

Akatswili a ndale ati A Mutharika akutsogolera bwino Malawi
06:24