Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Osangalatsa anthu pa masamba a mchezo ku Malawi akumana ndi akulu a Meta

View descriptionShare
 

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
832 clip(s)
Loading playlist

Akulu akulu a meta  amchigawo cha  ku m’mwela, kwa Africa ali mdziko la Malawi komwe akukumana ndi anthu ochita za msangalutso kapena kuti content creators pa masamba a mchezo komwe akambilane zokuti anthuwa azilipidwa ndalama ndi kampani ya Meta pa zomwe amaponya pa masamba a mchezo. Jayne Chilimampunga anali nawo ku nkumanowu ndipo wabwela ndi ripoti ili.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 975 clip(s)