Akulu akulu a meta amchigawo cha ku m’mwela, kwa Africa ali mdziko la Malawi komwe akukumana ndi anthu ochita za msangalutso kapena kuti content creators pa masamba a mchezo komwe akambilane zokuti anthuwa azilipidwa ndalama ndi kampani ya Meta pa zomwe amaponya pa masamba a mchezo. Jayne Chilimampunga anali nawo ku nkumanowu ndipo wabwela ndi ripoti ili.

Venancio Mondlane wati anthu alile maliro a Anselmo Vicente ku Mozambique
05:46

AIPAC ku Zambia yatsuta kuwunika ma bilu pomwe paliyamenti itseke pa 15 May 2026
10:17

Anthu 7 aphedwa ku Malawi pogawaganizila kuti akusowetsa maliseche
05:25