Sipikala wa nyumba ya malamulo ya mdziko la Malawi Sameer Suleman wakhazikitsa committee yatsopano yapadela yomwe ichite yakafuku fuku wa ngozi yomwe inapha wachiwiri kwa president Dr Saulos
Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu ndipo ku committee imeneyi mukhala aphungu oyima pa okha ndi aphungu a zipani za DPP, MCP, UTM ndi UDF . Mtolankhani wa Channel Africa Jayne Chilimampunga wabwela ndi nkhani yonse

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11

Mchitidwe wa uchifwamba ukuchulukila ku Malawi
06:53