Ngozi za pa nsewu zikupitilira kukwera mdziko la Malawi, ndipo pali mafunso pa zomwe zikupangitsa izi. Anthu ambiri akutaya miyoyo yawo ndipo ena akubvulala modetsa nkhawa. Mtolankhani wa Channel Africa Jane Chilimampunga, walankhula ndi katswiri pa nkhani zosiyana siyana mdzikolo Bernard Mwanza, yemwe wakhala akuinika mwa chidwi pa nkhaniyi.

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi
07:17

Alimi ena ku Zambia akudikilabe boma liwapatse malipiro atagulitsa mbewu ku FRA
07:55

Akatswili a ndale ati A Mutharika akutsogolera bwino Malawi
06:24