Nduna ya za chuma mdziko la Malawi Sausten Gwengwe akuchititsa misonkhano mmizinda yamdzikolo komwe akukambilana ndi akulu akulu a mabungwe osiyana siyana ndi cholinga chomva maganizo awo pa zomwe boma likuyenela kuchita mchaka chino cha 2023 kuti chuma chiyambenso kuyenda bwino.

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11