President wa dziko la Malawi Dr Lazarus Chakwera,anatsogolera a Malawi pa mwambo okumbukila malemu Saulos Chilima yemwe anali wachiwiri wawo ndipo mwambowu unachitikira m’boma la Mzimba pamene akubanja nawo anali ndi mwambo ngati omwewu ku kumudzi kwa Chilima m’boma la ntcheu. Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11