Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mwala wa Phosphate opangila feteleza wapezeka ku Zambia

View descriptionShare

Maboma a Sinda ndi Petauke ku chigao chakum’mawa cha dziko la Zambia apezeka ndi migodi ya mwala wa phosphate. Mwalawu umagwiritsidwa ntchito kupanga feteleza ndipo Gulu la makampani la  Wonderful Group of Companies lidzasonkhanitsa ndalama zoposa 2.5 billion US dollars pakukopa makampani akunja kwa dziko kuti adzathandize kukumba mwalawu. Daniel Elisha Banda ali ndi nkhaniyi.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 955 clip(s)