Mtsogoleri wa dziko la Zambia Hakainde Hichilema, wafotokoza kuti azimai ndi nsanamira zofunikira kwambiri pa zitukuko za dziko. A Hichilema analankhula mauwa dzulo pa mwambo wokumbukira tsiku la amai pa dziko lonse lapansi limene cha pamutu chake chinali motere: Danga, Chilungamo, Kuchitapo Kanthu, Kwa Amai ndi Atsikana Onse . Daniel Elisha Banda ali ndi nkhani yonse.

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11