President wa dziko la Malawi Professor Arthur Peter Mutharika, watsutsa mphekesera zokuti akudwala mwakaya-kaya ndipo wapititsidwa ku Chipitala mdziko la South Africa.Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka wadza ndi zambiri.

Venancio Mondlane wati anthu alile maliro a Anselmo Vicente ku Mozambique
05:46

AIPAC ku Zambia yatsuta kuwunika ma bilu pomwe paliyamenti itseke pa 15 May 2026
10:17

Anthu 7 aphedwa ku Malawi pogawaganizila kuti akusowetsa maliseche
05:25