Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mtsogoleri wa Malawi Arthur Mutharika wakana mphekesela yokuti akudwala

View descriptionShare
 

President wa dziko la Malawi Professor  Arthur  Peter Mutharika, watsutsa mphekesera zokuti akudwala mwakaya-kaya ndipo wapititsidwa ku Chipitala mdziko la South Africa.Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka wadza ndi zambiri.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 975 clip(s)